The Very Best - Hear Me lyrics

Published

0 94 0

The Very Best - Hear Me lyrics

Chichewa Siyani dumbo Siyani umbombo Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale? Siya umbanda Siya zauchigawenga Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi? Siyani dumbo Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Siya kaduka Siya zokonda kuba Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo Siyani kugona Siya kugona tulo Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka? Siya kaduka Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Hear me now Dzaka makumi asanu Zatha kufika lero Mpaka lero umphawi Ukungophabe dziko Dzaka makumi asanu Zatha kufika lero Mpaka lero umphawi Ukungophabe dziko