Pecca - My First Love lyrics

Featuring ,

Published

0 125 0

Pecca - My First Love lyrics

Yeah! P! Pecca on it Eyo Rina Leggo (Verse 1 'Pecca) We started way back, 2010, at the college/ She was a pretty lady full of love and care/ I used to call her Mami, she used to call me Papi/ A perfect match just like Jigga and Beyoncè/ Sankandikwana olo titakhala tsiku lonse/ She was a shooting star, ankawala kulikonse/ It was like a dream, i was living in my fantasy/ Ndipo nkhani ya break-up to me it was just a fallacy/ Makutu ndinaatseka zawina sindinkamvera/ Maso anga kutseka zawina sindinkapenya/ Living a good life yeah ngati ndikulota/ Mtima wa nzako ndi tsidya lina, mphuno salota/ Anandisiya, kundinyoza akuti ndine zoba/ Pamaso pama'friends ndinaonekadi zoba/ I shed so many tears maybe to forget her/ Pano nthawi yadutsa koma ndizosatheka/ #Hook (Katrina) My first love was so amazing She was so nice got me feelin' like a blessing But she lied to me And she break my hea-a-a-rt (Verse 2 'Pecca) December 2012, then i heard of her wedding/ I felt pain deep inside me, my heart was breaking/ How could she play with my heart just like solitaire?/ My heart, my soul, were broken beyond repair/ She changed numbers, changed numbers friends and blocked me on facebook/ Begun a new life when when my life was gradually ending/ The game was over, i was a loser, she was a winner/ My friends told me "dont worry man mupeza wina"/ Pena ndimazifunsa "Kodi zinalembedwa, kapena ndi tsoka chabe chinyau nkusemedwa?/ Poti konse ndingapite ndikumangosekedwa/ Ndasanduka chitonzo ndikumangonenedwa/ But whatever it takes i will be okay, i will be alright/ Its part of life, got me feeling like i am Dan Lu/ Pretty girls lie, mayne i feel Trey Songz/ Easy come, easy go, i feel like Bruno Mars/ #Hook (Verse '3 -Pecca) Ndifunseko, "kodi chimakhala chani atsikana?/ Kusiya mwamuna wabwino kuvomera tambwali/ Kuona mawanga akhanga mpaka kutaya nkhwali/ Nkumagawana mwamuna ndi zibwenzi zam'mbali/ Nde akakuvula amakusiya ukulira/ Tsoka ndilo matenda amakukhuthulira/ Zoti unali duwa lake izo amaiwala/ Umakhala utaguga, utayamba kudwala/ Panga chisankho lero usazanong'oneze bondo/ Ati ndine wamisala koma n'naona nkhondo/ Chikondi chomwechi ena takhetsera misonzi/ Kulumidwa ndi chakuda mpaka kukhetsa misonzi/ But thanks to Catherine for being there/ Everytime i need my best friend, she's always there/ Kundipukuta misonzi yanga ndikamalira/ Kundiuza "umu ndimmene moyo umakhalira"/ #Songwriters Pemphero Kapamba & Catherine