Nesnes - Wina Watenga lyrics

Published

0 377 0

Nesnes - Wina Watenga lyrics

WINA WATENGA Nesnes yeah pepa pepa koma wina watenga Uuuu oh iwe wina watenga pepa pepa Kusakongola kwanga kuja iwe wina wandikonda Kupanda ndalama kwanga kuja wina akuti sikupanda chikondi Chikondi unkandimana chija iwe wina wandipasa Tsono usandisokonezeso CHORUS Iwe wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga chikondi unkachikana chija Imva wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga pepa pepa Sataye thawi kundiyimbila moni wako sindiwusowa Sataye thawi kundiganizila za iwe nayiwala Chipongwe unkandipanga chija wina akundipasa ulemu Abale unkawa nyoza aja wina akuwapasa ulemu Chikondi unachithawa chija iwe wina wachikonda Ndalimba mtima ine hey CHORUS Iwe wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga chikondi ukachikana chija Imva wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga pepa pepa Oh oh chikondi cheni cheni ndachipeza ine Oh oh no sindifuna kubwelelaso mbuyo ine no no Malo ako wina watenga chikondi unkachiseweresa chija Iwe wina watenga Oh oh chikondi cheni cheni ndachipeza ine oh oh Sindifuna kubwelelaso mbuyo ine yeah CHORUS Iwe wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga chikondi ukachikana chija Imva wina watenga malo ako baby Ndati wina watenga pepa pepa