Langwan Piksy - Wako Wako lyrics

Published

0 240 0

Langwan Piksy - Wako Wako lyrics

VERSE 1 Uthenga wa masankha kwa Namazanje Panopa tiri official si za masanje Lero sitisamala za wansanje Tivine ingoma Mkhetekete ndi manganje CHORUS Tinafunitsitsa banja titamanga Koma tinadziwa kufika si ku thamanga Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako VERSE 2 Ulendo wathu tangoyamba komano tikafika Kaya mitunda tikwera ndi 0p titsika Tilowa pena mmatope pena tiponda minga Koma chimodzi ndikhulupira Yehova ndi Linga Tiyenda mu dzuwa Mvula Limodzi tikula Ukumva? Namazanje CHORUS Tinafunitsitsa banja titamanga Koma tinadziwa kufika si ku thamanga Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako VERSE 3 Poti ndasankha iweyo kuti ndikupatse wanga mtima Poti ndasankha iweyo kaya mokhwepa ndi mothina Honey ndasankha iweyo kaya kuwala kaya mdima Ine ndasankha iweyo kuti tikhale mpaka muyaya Ndasankha iwe Poti ndasankha iwe Poti ndasankha iweyo honey Ndasankha iweyo Namazanje CHORUS Tinafunitsitsa banja titamanga Koma tinadziwa kufika si ku thamanga Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako Ona lero ndine wako wako Ndine wako wako