Langwan Piksy - Mpaka Udzipita lyrics

Published

0 346 0

Langwan Piksy - Mpaka Udzipita lyrics

Ndikudziwa kuti ndafika mammawa Ndikudziwa zaku bhowa Yeah mtima wako ukuwawa Koma babe ukudziwa za ku bhawa Ndimakupeza wagona Sticheza ngati banja Ine Ndimakhala ndatopa Lonseli ndi vuto langa Mammawa uliwonse ukumalira Lero Ndakupeza ukupakila Komano honey just hold on I know I've done wrong Komazi ndi zazing'ono Nde CHORUS Mpaka udzipita Sindufuna kusikidwa. Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa Yes I know I didn't give you much attention Lately Every time on the cellphone Too much what'sapp, too much twitter Umafuna kundikonda koma sinkupasa mita Busy ntchito weekend ndi anzanga Ndimalonjeza zinthu zochuluka simpanga Umadandaula koma mmaiwala nsanga Kuchitenga for granted chikondi chomwe umandipatsa Mmalo molowera mmwamba I know we going down Ndikale lomwe ndinayenda nawe mtown Komano honey just hold on I know I'm doing wrong Komazi ndi zazing'ono Nde CHORUS Mpaka udzipita Sindufuna kusikidwa. Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa Usayese ndikutenga simple Kwa ine utanthauza dziko Chikondi chako chindipasa dzitho Ndikamati ndine mphongo ndiwe I swallow my pride ndameza matama Ndameza zochuluka pa kamoz Ndatsamwa Ndiri ndi munda koma sinkupalira Ndikudziwa sukukondwa mmomwe zikukhalira Ndiwauza anzanga ino weekend Sindioneka poti ndikhala ndiwe Eh yah ndikhala ndiwe baby Sindilora upite CHORUS Mpaka udzipita Sindufuna kusikidwa. Zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa