Khido - Zimandithekera lyrics

Published

0 172 0

Khido - Zimandithekera lyrics

[Intro: Khido] Hood Crunaz....! B2 on the board...! On the beat...! [Verse 1: Khido] Though they be hating, ngakhale athoke sh** Me still on my grind, yeah I be on my feet I step on the scene hot, n***as couldn't handle me I see them haters mad when me and my boys cheering D-sk**s cheering Ndimaziwa amangaza n'zomwe ndimachita, amafuna atapanga zomwe ndimachita Machick kufuna n'tawachita zomwe ndimachita Ndilipatali, mughetto ndafilidwa ngati soft ya-ganja Tsono bwana hater, nothing you can do on the boy "just quit" Mfana anakunamiza, no such thing like we all equal boy [Hook: Zizwa] I know you're hating And I know you're talking sh** Am still on my grind, still on my feet (Ndimapanga zanga ndipo zimandithekera) Yeeeaay.... (Ndimapanga zanga ndipo zimandithekera) [Verse 2: Lil Spy] It's my new style, and I don't give free-style You're busy talking sh** but I don't Wanna smile Focus on the future, osableya listen This is not a scripture, scripture or saplano I am on fire, koma sindikuspya I do it like magic, mafana mukunama Ndimakakamira flow mpaka ndikukana Swagger is in my intestine, you will never see me scratching like disc ya baseline Siine Tay Grin koma nane ndabwera, ndichiflow chamunthaka chodzusa mizimu kumanda Zikuchokera mmutu mwanga Izizi sizamihau [Hook] [Verse 3: Kab G] Shasha ndi shasha Ndimazimva sure ngati mfana wapa-heven Kuchedwa kumandikamba, koma sizindikhuza Ndine dolo, mfana wamakani Lusoli ndi talent, ndine number one Olo mutati, ndichiteko resign Mafana ndi-mafana, sangazafike paine Ndawapezera chochita, ndawaika paban Ndine mfana ozimva, ofilidwa ndi-akaziwa Ndani apa zaine m'ghetto ndiye saziwa Mfana ophaka life Muhip-hop game, still on the move Sindikutheka ngakhale athoke sh** My flow so bigger [Hook]