Verse 1: (krazie g) Fans ndimaibanda ngati ganja ndikupotayi Ndili nayo yambirimbiri ili nthumba mwa 3 quarter'yi (ah iwe sitikukamba zimenezo) eish oh ayi (Tikukamba za chilembwe) oh n'dala wa botayi Ndimamusaka ngati azungu amene anamupha Ndikampeza celebration pali ponse kudumphadumpha Ndimayesesa daily apezeke nthumbamu Nde dolla zosaka ku Lilongwe kuchita kutuwa mbu I want ronaldo, messi money, nike, addidas Ngati ili nkhani ya dollar ndipange add basi Make mad thousands and call em crazy G's I make crazy millions and call em amazing me Ndikudya paper koma akumva kuwawa ndi wina Ndikudya Esther lero koma mawa ndi Tina Siine wama looks ndine nkhwangwa Koma akazi ndi nkhuni ndimaawaza Chifukwa cha chilembwe wanga (revolver) Ndikusaka m'busa uja in a khakhi suit If you see him chonde mundiwuze ali kuti No h*mo but i love him like a choir Sindigwanda chilembwe olo atakhala Wakale, wokwinyika ngakhale wong'ambika Olo ali wonyowa ine ndimuyanika Sinditha kuphika but damn ndikuphula Funsa mng'ono wa bebi yanga, ndikudya moola Coz i stay on my grind like am s'possed to Kufuna jc ngati ndili mu form 2 Thats john chilembwe, mng'ono wa kamuzu Mkulu wa Gomani, best friend wanga uyu Ngongole sindibweza, ndikasanja ndimasowa Mzinda wandikwana ndikulowela ku Dowa Alipo ambiri ma man onditchesa Lero akafika pa yard sandipeza Ndikuteteza Chorus: (tanaposi & krazie G) John chilembwe John chilembwe Jo-jo john chilembwe John chilembwe Amapoilira john chilembwe uyu Akupoilira john chilembwe Verse 2: (martse) Ma heroe ndimaasaka john chilembwe ndiwoyamba And now i'm switching gears nduhasa kamuzu banda Having money is an option all i had to do is choose Sindimalamulidwa nde sindikhala mmaluzi This aint no lie John chilembwe wako ngwa china, wameta mohawk, wavala tie Wa ine ndi brand new for zibagi, dubai Ndine tholo ndi kale nde ndimangokhala high Martse ndi mfana wotentha nde palibe akuti nyo Ndine mtumbuka wosamba mphwanga, you already know Nde mukamakambakamba za john chilembweyo Waine ali ngati dstv, so much more You dig (hypa) Dolla zanga ndizama looks ndiyeno fans imangokongola Fans yakunyasa imabwela kuzangokongola Dolla zimathoka koma ine ndili phe Iwe zako kungothoka uwone tulo ndiliphe Ndikufuna kunenepa nde ndikungodya zi money Ku chipatala andiwuza ndizidya ndisazimane Kuthoka ndi chilembwe timatchila mwa kathithi Ngati dolla zimathoka iwe zako nzachibwibwi I'm sick with the money dolla zanga zingofwenthila Ndinkona ndimaziblowa ndikazimva zikufwenthila Anijo kundiyabwa ndimangokanda ngati Bongo man Koma kundipempha ndimangokana ngati Ntaba man Nkhani za chilembwezi zilibe chibale Olo Faith zamakwachazi alibe chibale Dolla zanga zimathokadi, zimapanga noise Iwe zako kusokosa ndekuti wagwetsa ma coins (back to chorus) Verse 3:(judagaga) I keep it old school, john chilembwe yekha yekha Kamuzu ali bho koma nthumba akumachepa Ndikasanja dolla ndimafuna fans idziwe Mahope n'nawathoka kuti nawonso adiwe Get his face on a bank note nde ndizamulora Dead people got my number coz dolla zikundikhola I get money by all means even change chaku msika Chilling with dead people thats why my flow is mad sicker Ndimamukonda john chilembwe, you can call me haida Cause when i have him in my pockets i'm sipping ciders In love with this black man in a khakhi suit Siine mzungu koma nane ndimamuhanta ndi mifuti My account got much figure kuposa akazi Dirty money yaku Malawi, john chilembwe wa magazi Get my money in my bra ngati recka sungandibele Ndimazakuwa kuti HUH nanenso ndizamufele (back to chorus)