Revolver - Bagi Party lyrics

Published

0 133 0

Revolver - Bagi Party lyrics

Chorus (revolver) Its a bagi party Cheka chibukucho tiyake Utha kubwela usanadye Chifukwa its a bagi party Verse 1 (stich fray) Bring no bottle Mkunda, gin, wine kwanu konko Wachoka osadya uzidya mom'mo Mom'mo mom'mo mom'mo mom'mo Uzidya mom'mo mom'mo mom'mo mom'mo YEAH YEAH Tili kuno sitichoka Awuzeni amayiwo ubwele wokha wokha Wadzulo wadzana chifukwa sitivokha Tinabadwa nazo izi sizapompa YEAH Tili kuno sitichoka Awuzeni amayiwo ubwele wokha wokha Wadzulo wadzana chifukwa sitivokha Tinabadwa nazo izi sizapompa YEAH EH (AHHH IWE) mundibudulira Mundibudulira, bwino bwino, bwino mundibudulira (AHHH IWE) mundibudulira Mundibudulira, vina bwino iwe undibudulira (chorus) Verse 2 (judagaga) Its a friday night, fans ikulowa out Green, special, stout, koma zoti ndivaya i doubt Am at my joint ku nancholi Fans imanditcha ka duli Bagi ndi number one Anganditsuse ndani Ena atathima thi, ndimangofila dim Ena akumwa zowawa ngati akumwa mandimu 2 mina ablakilatu Escom yathekelatu Thats when we start to party, call it the bagi party Vina osangoyima like a statue of liberty Thats when we start to party, call it a bagi party Thats when we start to party, call it a bagi party Thats when we start to party, call it a bagi party (chorus) Verse 3(revolver) Chapa den undipeze, tingosisa zi masese Muwuzeni mkazi wanga ngati wakwiya nazo athese Packet, no bottle Mabebi, no photo Tiyake tivokhe Tivine titote-le Gwila chibele bele bele belemuda Ponya chimwendo, lero sitichoka mpaka kucha Gwila chibele chibele bele belemuda Ponya chimwendo, lero sitichoka mpaka kucha Back to the drinking, ka bawa kumutu kayamba kuchepela Looking like tikumenya bwalo likule chifukwa tikumenya cirlular Sip, pa** sip, pa** tiki-taka Tingoyamba kufinyila tikachedwa kuyaka