Lawi - Galimoto lyrics

Published

0 155 0

Lawi - Galimoto lyrics

{Chorus} Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto) Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto) {Verse 1} Ndimayenda wapasi ine eh-eh Minga zimandibaya ine eh-eh Anthu akandiona ine eh-eh Amayamba kuseka ine eh-eh {Refrain} Kodi dona yambwana iyo (Siyo) Kubayika ndi minga iyo (Siyo) Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo) Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh {Chorus} Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto) Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto) {Verse 2} Poti bambo ndinu namalamba mimbayi ndi umboni M'mudzima nkhani akamakamba siyose ili miseche Muli ndi galimoto mumakwera mukafuna Nane ndi galimoto ndingathetse zolankhula {Refrain} Kodi dona yambwana iyo (Siyo) Kubayika ndi minga iyo (Siyo) Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo) Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh {Bridge} Sho sho, pee-pee Fumbi kuti lakata Sho sho, ka-kata boom, kata-kata bumba Vrrm, vrrm, pha Vrrm, vrrm-vrrm, pha {Refrain} Kodi dona yambwana iyo (Siyo) Kubayika ndi minga iyo (Siyo) Ngati makobidi kulibe kwawoko (Siyo) Ndalema ndi chitonzo mundigulire, oh {Chorus} (Sho sho, pee-pee, sho) Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto) Galimoto, galimoto (Ndidziti nkati break khwe miseche nayo balala) Galimoto, galimoto (Mundigulire ine galimoto)