KBG - Zoononga Moyo lyrics

Published

0 160 0

KBG - Zoononga Moyo lyrics

Verse 1:LAWI Amati bawa ndi njira yochotsela nkhawa nanga bwanji ukadzuka mmawa matsile maluzi uliso confused ndingonena chindunji chenicheni nchiti chokhalila mfiti when in actual sense you r a slave to the sin that yo glue to iwe tchimo litavala umunthu chonde ndithandizeni ndidziweko swaga as much as i know ndizoononga moyo wanga sikuzikweza kodi? Kuwalila kodi? Kukhutitsidwa ndimmene ndavalila kodi? Inde asungwana apapa mukukhwana titha kuyamikila mpakana kupanga mwana Inde abwana mwatchena osanama but check on the . . . Ndiyesu mwasemphana u can be who u want to b multiply zinthu ngati tyms u can buy evrything with paper but heaven uuuh uuuh zachisoni pepa {Chorus:} kodi wapindulanji iweyo utapeza zonse zofuna mtima wako koma zonse zomwe wapezazo mulibe chipulumutso ndizinthu zoonona moyo wako x2 Verse2:KBG lawi nane ndiwauze fanzi . . . .