[Chorus-Sir Patricks]
Chikondi ndichophweka ukapeza soul mate
Uzakhala wokoma moyo wako wonse
Ukazapeza namwali wachikondi ngati wangadi
Ngati wangadi yeah
Ndiwe number one (poti sukudziwa)
Ndiwe number one (uleke kulota)
Ndiwe number one (poti sukudziwa)
Ndiwe number one ndimawelengela
[verse 1-Revolver]
One, ndiwe one ngati Mata
Okuposa palibe iwe, ata
Olo zinthu zitavuta bwanji ndikakhala ndiwe m'mtima mumakhala bata
Two, ena kutokota timagontha nkhutu
Its just us two
Zima looks tho
Siwe nkhwangwa, no
Koma umandiwazatu
Dont you ever forget
You all that i need, no Meth
Nthawi zonse dzina langa limakhala mkamwa mwa anthu ngati colgate
Ndinkakhala ndi uyu lero mawa ndi wina
But you is a keeper ngati Pepe Reina
This feeling is new to me
Tabwela ndikuwuze what you do to me
(back to chorus)
[verse 2-Revolver]
You blow me away you the bomb bae
Uli hot ngati phwanya yaku bombay
I can look in those eyes all day
Game ndimaisata but i dont play
Ndinali player koma pano ndinabinya ah
Wofuna kulanda zimudinya ah
Mwini wake wa mtima wanga iwe
Umawala mu mdima wanga iwe
You see i dont love you coz i need you, i need you coz i love you
Olo nditaluza chili chonse i can still get through it as long as i have you
My love ain't blind
Imawona but it just dont mind
Eh ili sisewelo
Iwe wekha nzakuveka velo
(back to chorus 2x)