Yeah! P! Pecca on it
Eyo Rina
Leggo
(Verse 1 'Pecca)
We started way back, 2010, at the college/
She was a pretty lady full of love and care/
I used to call her Mami, she used to call me Papi/
A perfect match just like Jigga and Beyoncè/
Sankandikwana olo titakhala tsiku lonse/
She was a shooting star, ankawala kulikonse/
It was like a dream, i was living in my fantasy/
Ndipo nkhani ya break-up to me it was just a fallacy/
Makutu ndinaatseka zawina sindinkamvera/
Maso anga kutseka zawina sindinkapenya/
Living a good life yeah ngati ndikulota/
Mtima wa nzako ndi tsidya lina, mphuno salota/
Anandisiya, kundinyoza akuti ndine zoba/
Pamaso pama'friends ndinaonekadi zoba/
I shed so many tears maybe to forget her/
Pano nthawi yadutsa koma ndizosatheka/
#Hook (Katrina)
My first love was so amazing
She was so nice got me feelin' like a blessing
But she lied to me
And she break my hea-a-a-rt
(Verse 2 'Pecca)
December 2012, then i heard of her wedding/
I felt pain deep inside me, my heart was breaking/
How could she play with my heart just like solitaire?/
My heart, my soul, were broken beyond repair/
She changed numbers, changed numbers friends and blocked me on facebook/
Begun a new life when when my life was gradually ending/
The game was over, i was a loser, she was a winner/
My friends told me "dont worry man mupeza wina"/
Pena ndimazifunsa "Kodi zinalembedwa, kapena ndi tsoka chabe chinyau nkusemedwa?/
Poti konse ndingapite ndikumangosekedwa/
Ndasanduka chitonzo ndikumangonenedwa/
But whatever it takes i will be okay, i will be alright/
Its part of life, got me feeling like i am Dan Lu/
Pretty girls lie, mayne i feel Trey Songz/
Easy come, easy go, i feel like Bruno Mars/
#Hook
(Verse '3 -Pecca)
Ndifunseko, "kodi chimakhala chani atsikana?/
Kusiya mwamuna wabwino kuvomera tambwali/
Kuona mawanga akhanga mpaka kutaya nkhwali/
Nkumagawana mwamuna ndi zibwenzi zam'mbali/
Nde akakuvula amakusiya ukulira/
Tsoka ndilo matenda amakukhuthulira/
Zoti unali duwa lake izo amaiwala/
Umakhala utaguga, utayamba kudwala/
Panga chisankho lero usazanong'oneze bondo/
Ati ndine wamisala koma n'naona nkhondo/
Chikondi chomwechi ena takhetsera misonzi/
Kulumidwa ndi chakuda mpaka kukhetsa misonzi/
But thanks to Catherine for being there/
Everytime i need my best friend, she's always there/
Kundipukuta misonzi yanga ndikamalira/
Kundiuza "umu ndimmene moyo umakhalira"/
#Songwriters
Pemphero Kapamba & Catherine