{Intro} Ayy Chifundo nane Chifundo nane Oh, Chifundo nane Chifundo nane Chifundo nane Chifundo nane Mtima wanga don't you worry Everything is gonna be alright {Chorus} Ambuye ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Mtima wanga sudera nkhawa Chifukwa ali ndi chifundo nanee Ine mtima wanga sudera nkhawa (Oh no) Chifukwa ali ndi chifundo nane {Verse 1} Machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo Mutazindikira zamumtima mwanga mukhoza kumandisala Mutha kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m'ndende Ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa Ndiye amene anandipanga amandidziwa Zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika Koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe Amatsegura manja ake ndi kundikumbatira
{Chorus} Oh, ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nanе Mtima wanga sudera nkhawa Chifukwa ali ndi chifundo nanee Ine mtima wanga sudera nkhawa (Oh no) Chifukwa ali ndi chifundo nanе (Oh, yeah) {Verse 2} Ayi-yayi-yayi Ayi, ndachoka kutali, moyo wanga ndi umboni Wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete Pomwe adani anga andikumbira mitsinje Wandimangira mlatho, ndayenda powuma Wandifewetsera zolimba zanga {Chorus} Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ali ndi chifundo nane Ine mtima wanga (Sudera nkhawa chifukwa ali ndi chifundo nane) Ine mtima wanga (Sudera nkhawa Chifukwa ali ndi chifundo nane)