[Intro]
I know for so long you have been waiting for this one homie
I've bring it home
Its your boy Khido M kid on this one
Pages the mixtape
[Verse: Khido]
I ain't spitting fake things in my rhymes
I ain't talking about dreams or dissing fake hustlers
Magiga onyenyeka, hoping to be where am at
Am rolling to the top, never black and white dreams
Mafana kupanga zanga, nane still kupanga zanga
Double in my swag, ali blind sakujaja
Patali sakuona
My beats blowing up their mind, so they're scratching their medulla
They claim to go deep, but they have never catch my deeper thoughts
No matter how narrow, I will be flowing in your veins even in your arteries
And nothing you can do about it
Listen close, flow retarded
Anawa akasuta ndudu, kunja kuli dzuwa
Nkumazimva kutentha, amaona ngati afikapo
Kumbali amazipopa, akandiona ndikubwera amadzichepesa
Swagger yanga ndi-mvula ndiye ndimawanyowesa
Akandionera patali iwo amasintha njira, kudusa zachidule
Mafana kuithawa mvula
Nzoti ndili patali, ngakhale makanja pomwe ndili sangafike
Ndine mfana ovaya
Wekha sungaone kuti flow-yi ndi ganja, mafana ikuabanda ngati Rasta ku Zion
Funsafunsa tidayamba zinthuzi mpakale, now standing tall
Ona flow dongosolo
Kufuna atamaka koma sakuona nyatwa, am fast in this rap thing "chipolopolo"
Swagger like 6.4
Fresh in the zone, with the boys am cheering
Zachibwana njee, mafana kumangothawa
Nzoti paine sangamake, paliponse sangamveke
Amanditcha Khido ena nkumanditcha ninja, mwana osaimva
Kuphunzitsa mafana swagger kudzera muspeaker
Kumenya magiga daily, running the streets
Palibe chomwe ungandiuze, am the best in this
I've been a man in this like since D made me
So you can never stop me, just copy what I does
But if you copy it wrong, you gonna never impress them
They need impression
I got 'em hoochies at the club shaking it awesome
Dropping this mixtape, you'll be calling it awesome
This is just a demo, here am just cheering with tha kick, snare and symbols
Khido - Pages lyrics
Album Pages