Verse 1 Ulusi ngati asokera pompo Akuyenda slow slow ngati nkhono My girl is fine aaaaaah Look she is rocking Designer Savala za make Dzana Usiku kuwala ngati Masana ondipemphayo ine ndi mmana Chorus wendy iiiih iiih u look like Wendy iiiih iiiiih U look like Harawa ( Wendy) lero lokha ndikulawa (Wendy) sindidikilira mawa ( Wendy) A jealousy amva kuwawa Post Chorus Nkhani yovina palibe angamupose Kusekelera ngati akumenya pose too much juice Too much sauce my wendy Harawa Amatha Zonse X2 Verse 2 mkazi wabho mkazi wa nyatwa mkazi ofatsa mkazi wa bata mkazi odziwa amazitsata ndizakutengela kwamasten mkazi wa banja eeeeh ukudziwa babe ndizakutengera Chaku Nkhatabay Uzafile ka View umaziwa babe U my Wendy Harawa A nsanje amva bebe eeeh nde ana omwe uzandi balire mnakuuza kale kuti udalire
Chikondi Chokoma Chopanda Malire ndi Reason yokhayo ndizaku malire Chorus wendy iiiih iiih u look like Wendy iiiih iiiiih U look like Harawa ( Wendy) lero lokha ndikulawa (Wendy) sindidikilira mawa ( Wendy) A jealousy amva kuwawa Post Chorus Nkhani yovina palibe angamupose Kusekelera ngati akumenya pose too much juice Too much sauce my wendy Harawa Amatha Zonse X2 U look like Harawa ( Wendy) lero lokha ndikulawa (Wendy) sindidikilira mawa ( Wendy) A jealousy amva kuwawa Post Chorus Nkhani yovina palibe angamupose Kusekelera ngati akumenya pose too much juice Too much sauce my wendy Harawa Amatha Zonse X2 My Girl is fine aaaaaaaa wendy iiiih iiih u look like Wendy iiiih iiiiih U look like Harawa ( Wendy) lero lokha ndikulawa sindidikilira mawa A jealousy amva kuwawa