Abatiya - Zitakhala Chonchi lyrics

Published

0 227 0

Abatiya - Zitakhala Chonchi lyrics

VERSE 1 Titavaya koyezetsa nkundipeza nako ndekhaaaa Ntakhala osabereka ungakhalebe Dekhaaaaa? Ukandipepha dola masaka nkukupatsa Nditakhala ndimakaba ungakhalebe ofatsa? Ndimagona kwathu iwe umagona kwanu Stern yanga itakuuza Abatiya amabwebweta Iweyo ungalimbe kapena uthaaaaa kufoka Nditakha bawa ai koma fodya ndimakoka Umadziwa Fanz imakadya mahule Nditakha ndimava usiku uliwonse Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani Ndikufuna ndingodziwa chonde Undimasukire CHORUS /HOOK Undimasukire babieeeee Ndikufuna ndidziweeee yeeeh yeeeh Ndati pali zinthu zina zomwe sumadziwa mami Zokhudza ine zokhudza iweso Nanga nditakhala chonchi ungata? Nanga zitakhala chonchi ungata? Iweyo Ndikufuna ndidziweeeee Zitakhalaaaa chonchiii VERSE 2 Nditakhala sinkufuna koma iwe osamaona Ndimaganiza zaiwe pokha pokha nkakuona Kuti ndimalowa tchetchi kufuna Kunamizaa Pogonaso ndimakodza tulo sungalipeza Zitakha ndimakukonda cha zomwe ulinazo Kuti zosezi zitatha chikondi chidzatha Kwanu kumasowa nkhuku, nditakhala ndine Kuti zovala izizi sizaine zama friends Ndimadziwa umanyada kwa anzakoooo zaa ine Nditakhala ndimatamba usiku mawuruka Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani Ndikufuna ndingodziwa chonde Undimasukire BACK TO CHORUS/HOOK BRIDGE Nanga zitakhala chonchi ungata? Iweyo (Ndikufuna ndidziwe) Nanga zitakhala chonchi ungataaaaaaaaa? Ndikuna ndidziwe Ngati uli wa ineyoooo Babie yeahhhhhh Ndimasukile Ndikufuna ndidziweeeeeeeeeeeee BACK TO CHORUS/HOOK (X2)