Abatiya - Mupatse Nkono lyrics

Published

0 208 0

Abatiya - Mupatse Nkono lyrics

[Intro] Abatiya on this one Oh oh oh oh Ahhh Nah nah nah Eeeeeye [Chorus] NdiKusowa kwanga . Pamasowa pake (aku sa nduka Chitonzo) Anawaaaa Alera bwanji Opanda bambo awo pafupi Akasowa chakudya (Mupatse nkono) Akasowa chovala (Mupatse nkono) Akasowa pokhala (Mupatse nkono oooooooooh) Mmmmh [Verse 1] Zimathekaa akasowa nchere Amangogwetsa misonzi AkakumbukaaAaaa Moyo wake unali ophwekaaa Zoti angamapephe Iyeyu Sankayembekezera Koma kuchoka kwanga padziko Kunasitha nyengoo zakeee [Chorus X 2] NdiKusowa kwanga . Pamasowa pake (aku sa nduka Chitonzo) Anawaaaa Alera bwanji Opanda bambo awo pafupi Akasowa chakudya (Mupatse nkono) Akasowa chovala (Mupatse nkono) Akasowa pokhala (Mupatse nkono oooooooooh) Mmmmh [Verse 2] Amayesa ma bizinez (Mapeto ake amaduka) Nzeru nzake zinatha uyu Amalakalaka ndili moyo Anawonse apulukira (wa*kulu uja ndi Mbava) Ang'ono ang'o samuveraaaaa Sukulu anasiya kale kale [Chorus X 2] [Bridge] Mupatse nkono Mupatse nkono Mupatse nkono Eh