Ukakhala iwe mphwanga Usadzinamize uli ndi abale Amakukonda uli ndi chuma Ukasauka kukutaya Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi Iwe iwe mvera Tchera tchera khutu Ganiza ngati munthu