CHORUS Bwera Pafupipi Lady undigwire Chiuno Changa. Usavine dance yakunja koma ya komkuno ku nyasa. Umandiwaza chifukwa chikhalidwe suiwala. Soon i will take u back tivine ka dance timavina tili mafana. Kadi Kadi, Kadi Kadi, kadigong'oooo (bwera tivine) Kadi Kadi, Kadi Kadi, kadigong'o (ndi iwe)