[Intro] I know for so long you have been waiting for this one homie I've bring it home Its your boy Khido M kid on this one Pages the mixtape [Verse: Khido] I ain't spitting fake things in my rhymes I ain't talking about dreams or dissing fake hustlers Magiga onyenyeka, hoping to be where am at Am rolling to the top, never black and white dreams Mafana kupanga zanga, nane still kupanga zanga Double in my swag, ali blind sakujaja Patali sakuona My beats blowing up their mind, so they're scratching their medulla They claim to go deep, but they have never catch my deeper thoughts No matter how narrow, I will be flowing in your veins even in your arteries And nothing you can do about it Listen close, flow retarded Anawa akasuta ndudu, kunja kuli dzuwa Nkumazimva kutentha, amaona ngati afikapo Kumbali amazipopa, akandiona ndikubwera amadzichepesa Swagger yanga ndi-mvula ndiye ndimawanyowesa Akandionera patali iwo amasintha njira, kudusa zachidule Mafana kuithawa mvula
Nzoti ndili patali, ngakhale makanja pomwe ndili sangafike Ndine mfana ovaya Wekha sungaone kuti flow-yi ndi ganja, mafana ikuabanda ngati Rasta ku Zion Funsafunsa tidayamba zinthuzi mpakale, now standing tall Ona flow dongosolo Kufuna atamaka koma sakuona nyatwa, am fast in this rap thing "chipolopolo" Swagger like 6.4 Fresh in the zone, with the boys am cheering Zachibwana njee, mafana kumangothawa Nzoti paine sangamake, paliponse sangamveke Amanditcha Khido ena nkumanditcha ninja, mwana osaimva Kuphunzitsa mafana swagger kudzera muspeaker Kumenya magiga daily, running the streets Palibe chomwe ungandiuze, am the best in this I've been a man in this like since D made me So you can never stop me, just copy what I does But if you copy it wrong, you gonna never impress them They need impression I got 'em hoochies at the club shaking it awesome Dropping this mixtape, you'll be calling it awesome This is just a demo, here am just cheering with tha kick, snare and symbols